Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani
Ndi ntchito ya manja anu
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani
Ndi ntchito ya manja anu
Ine ndiza
Kuimbirani
Ndikadali ndi moyo
Ndizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
Ine ndiza
Kuimbirani
Ndikadali ndi moyo
Ndizalemekeza inu
Ndi umunthu wanga onse
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani (oh)
Ndi ntchito ya manja anu
Ulemelero wanu
Ukale nthawi zonse
Ambuye
Kondwelani
Ndi ntchito ya manja anu
Oh, ife tiza
Kuimbirani
Tikadali ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wathu onse
Ife tiza
Kuimbirani
Tikadali ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wathu onse
Ndipo Mulungu
Agade
Agade
Agade, agade
Mulungu agade
Salephela Ana
Iye Mulungu
Agade
Agade
Agade, agade
Mulungu agade
Salephela Ana
Kodi ndiye
Alefa, Omega
Oyamba, osiliza
Wachipulumutso cha moyo wanga
Oh, Iye Mulungu
Agade
Agade
Agade, agade
Mulungu agade
Salephela Ana
Iye ndiye
Alefa, Omega
Oyamba, osiliza
Wachipulumutso cha moyo wanga
Oh, Iye Mulungu
Agade
Agade
Agade, agade
Mulungu agade
Salephela Ana
Munalenga munthu
M’chifaniziro chanu
Ambuye
Kondwelani ndi ntchito
Ya manja anu
Munalenga munthu
M’chifaniziro chanu
Ambuye
Kondwelani ndi ntchito
Ya manja anu
Ife tiza
Kuimbirani
Tikadali ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wathu onse
Ife tiza
Kuimbirani
Tikadali ndi moyo
Tizalemekeza inu
Ndi umunthu wathu onse